Mkangano wabuka m’banja la a Gondwe pa za munthu yemwe akuyenera kulowa ufumu wa Chikulamayembe. Mpungwepungwewu wayamba potsatira imfa ya Walter Gondwe, yemwe adali…
Mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika Lachinayi adachenjeza mtsogoleri wa chipani cha MCP Lazarus Chakwera ponena kuti akukolezera zipolowe za ndale. Koma Chakwera, polankhula…
Mtsogoleri wa chipani cha UTM Party Saulos Chilima wati pulezidenti Peter Mutharika sakuyenera kulamulira dziko komanso wapampando wa bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC)…
Yemwe adaimira chipani cha MCP, Lazarus Chakwera, dzulo adati sakuvomereza chisankho cha pa 21 May, ponena kuti adaberedwa mavotiwo. Polankhula kwa atolankhani kulikulu la…
Peter Mutharika, yemwe adapambana pa chisankho cha pa 21 May, dzulo adapempha Amalawi kuti apite patsogolo ndi kukhala wogwirizana ndi a mtendere potukula dziko…
Pamene alimi ena akugulitsa ziweto zawo kwa mavenda motsika mtengo, Chawezi Nyirenda yemwe ndi mlimi wa nkhumba ku Lilongwe akupha makwacha a nkhaninkhani popha…
Bungwe la Water for People Malawi (WPM) lomwe cholinga chake n’kuonetsetsa kuti anthu m’dziko muno azimwa madzi aukhondo, komanso kukhala ndi zimbudzi zabwino lati…
M’mwezi wa February chaka chino mlimi wina wa nkhumba m’boma la Lilongwe, Jeofrey Kaiyatsa, adaona ngati malodza nkhumba zake zonse zitafa ndi chigodola. Panthawiyo…
Khungu ndi amodzi mwa matenda a maso opeweka. Katswiri wa maso pa chipatala cha Chiradzlu Frank Mwamadi wati izi zimachitika munthu akasamalira bwino maso…
Zipani za Democratic Progressive Party (DPP) ndi UTM zati zakhumudwa ndi kalata yomwe Sinodi ya Nkhoma ya mpingo wa CCAP yatulutsa sabata yatha. Kalatayo,…
Pamene mbewu ya mtedza yacha, katswiri wa mbewu za mtunduwu kwa Bvumbwe Richard Andasiki akuti alimi ateteze mbewuyi ku chuku pamene akukolola, kuyanika, kusenda…
Woona za mafizo pa chipatala cha anthu achikulire cha Kalibu ku Lilangwe m’boma la Blantyre Veronica Mughogho akuti mafizo ndiothandza kwambiri pa miyoyo ya…